π
₯οΈπ
οΈπ
‘οΈπ
’οΈπ
οΈ π
οΈπ
οΈπ
οΈ
Hey girl ,whats yo name//
Kandiuza priscilla//
Ine kukaona mmaso mwake ndakaona kut kakulila//
Ndakafusa vuto nchani
Kandiuza ndizitaye
Then kuyamba kucheza
Kumenya ma jokes aa kaseka
Ndati akaka katheka ndingolimbikila mwina tigwila
Kazamdipasa number yak kandiuza kuti kandiimbila (hello)
Ife man kufusila
Man kandikweza njinga
Akuti ndikhale bestie panopa sikakufuna zodater
π
οΈπ
‘οΈπ
οΈ π
οΈπ
οΈπ
οΈπ
οΈ
I know ulibe guy u ar heartbroken
Paja ena ankakucheater koma thats oky
Ndungofuna uiwale zima ex
Sinzakuplayer paja ineyo messi
π
οΈπ
οΈπ
οΈπ
οΈ
Iwe bestie Uzingodikila
Iwe bestie, iwe tadekha
Iwe bestie, ndiwe wekha
Iwe bestie uzingodikila
π
₯οΈπ
οΈπ
‘οΈπ
’οΈπ
οΈ π
£οΈπ
¦οΈπ
οΈ
Kamandicaller ndivaye paden
Kakutenge tizikachileller
Kamandipempha kagone paden kakaona kukuzizila
Pa uyu sindingagive
Ma hope nonse mundimve
Chimbina chokhacho kunjanja
Iwe wekha ndi wa banja
You gat a booty that i wanna die for
Wina kulanda nxamuthyola spinal
Umandifila sungakane i know
Koma zodeta umandiuza ayi no
Bebie tiziti sundifuna , sukufuna ku dater chi ndi rapper chobhebha
Chinfana chowala, chimfana cha gheli,chimfana cha dollar, chimfana cha high choyenda ndi bola ππ‘π’π¦πππ§π ππ‘π π‘π’π π‘ ππ‘π¨π²ππ§ππ π§ππ’ ππ¨π₯π
Kapena ufuna ndigwile kanzako
Ndiziyenda nako povaya ku show
Ndisiye kuyankha ma call
Kubwela paden so no
Simukupanga za bho
Bebie ukupanga zobhowa
Ndatopa kudikila
No more kupilila
Bebie wandilila
Outro(Esther chimwala)
Bestie please understand me , i need time to heal before i seriously date again, u know i love youπ₯° but we cant date as of now , am still heart broken π . Dont be mad at me, am not ready to lose you as my bestie. I love you heavy. Gimme time please